-
Oweruza 16:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Poyankha Samisoni anamuuza kuti: “Atandimanga mwamphamvu ndi zingwe zatsopano zimene sanazigwiritsepo ntchito, ndingafooke ndi kukhala ngati munthu wamba.”
-