Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno mu Betelehemu+ wa ku Yuda munali mnyamata wina, wa m’banja la Yuda, ndipo anali Mlevi.+ Iye anakhala kumeneko kwa kanthawi.

  • Oweruza 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kuwonjezera apo, Mika anapatsa mphamvu Mleviyo+ kuti atumikire monga wansembe+ wake ndi kupitiriza kukhala m’nyumba ya Mika.

  • Oweruza 18:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kenako ana a Dani anadziimikira chifaniziro chosema+ chija, ndipo Yonatani+ mwana wa Gerisomu,+ mwana wa Mose, pamodzi ndi ana ake, anakhala ansembe a fuko la Dani kufikira tsiku limene anthu a m’dzikolo anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena