Genesis 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Akapolowo ndi ana awo anawaika patsogolo penipeni,+ Leya ndi ana ake anawaika pakati,+ ndipo Rakele ndi Yosefe anawaika pambuyo.+ Deuteronomo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anakumana nanu panjira ndi kupha anthu oyenda movutika m’gulu lanu amene anali kumbuyo. Iwo anachita izi pamene munali olefuka ndi otopa ndipo sanaope Mulungu.+
2 Akapolowo ndi ana awo anawaika patsogolo penipeni,+ Leya ndi ana ake anawaika pakati,+ ndipo Rakele ndi Yosefe anawaika pambuyo.+
18 Iwo anakumana nanu panjira ndi kupha anthu oyenda movutika m’gulu lanu amene anali kumbuyo. Iwo anachita izi pamene munali olefuka ndi otopa ndipo sanaope Mulungu.+