Genesis 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele, ndipo anam’konda kwambiri Rakele kuposa Leya.+ Motero anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+
30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele, ndipo anam’konda kwambiri Rakele kuposa Leya.+ Motero anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+