Genesis 31:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Ndiyeno Labani anadzuka m’mamawa n’kupsompsona+ adzukulu ake ndi ana ake aakazi ndipo anawadalitsa.+ Atatero, ananyamuka kubwerera kwawo.+ Machitidwe 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo onse analira kwambiri, ndipo anakumbatira+ Paulo ndi kumupsompsona mwachikondi.+
55 Ndiyeno Labani anadzuka m’mamawa n’kupsompsona+ adzukulu ake ndi ana ake aakazi ndipo anawadalitsa.+ Atatero, ananyamuka kubwerera kwawo.+