Salimo 119:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ine ndine mnzawo wa anthu okuopani,+Ndiponso wa anthu osunga malamulo anu.+