2 Samueli 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako mfumu inauza Itai+ Mgiti kuti: “Kodi iweyo ukupita nafe chifukwa chiyani? Bwerera+ ukakhale ndi mfumu, pakuti ndiwe mlendo komanso ndiwe wothawa kwanu.
19 Kenako mfumu inauza Itai+ Mgiti kuti: “Kodi iweyo ukupita nafe chifukwa chiyani? Bwerera+ ukakhale ndi mfumu, pakuti ndiwe mlendo komanso ndiwe wothawa kwanu.