Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Boazi anamuyankha kuti: “Ndamva zonse zimene wachitira apongozi ako chimwalilireni mwamuna wako.+ Ndamvanso kuti unasiya bambo ako ndi mayi ako, komanso dziko la abale ako, n’kubwera kuno kwa anthu amene sunali kuwadziwa n’kale lonse.+

  • Esitere 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 M’zigawo zonse ndi m’mizinda yonse kumene mawu a mfumu ndi lamulo lake linafika, Ayuda anali kusangalala ndi kukondwera. Anachita phwando+ ndipo linali tsiku lachisangalalo. Anthu ambiri+ a m’dzikomo anayamba kudzitcha Ayuda+ chifukwa anali kuchita mantha kwambiri+ ndi Ayudawo.

  • Salimo 45:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwe mwana wanga wamkazi, mvetsera ndipo ona ndi kutchera khutu.

      Uiwale anthu ako ndi nyumba ya bambo ako.+

  • Yesaya 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti Yehova adzachitira chifundo Yakobo+ ndipo adzasankhanso Isiraeli.+ Iye adzawapatsa mpumulo m’dziko lawo.+ Alendo adzakhala nawo limodzi ndipo adzadziphatika kunyumba ya Yakobo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena