Mateyu 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano atalowa mu Yerusalemu,+ mzinda wonse unagwedezeka. Ena anali kufunsa kuti: “Kodi ameneyu ndani?”
10 Tsopano atalowa mu Yerusalemu,+ mzinda wonse unagwedezeka. Ena anali kufunsa kuti: “Kodi ameneyu ndani?”