Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+
21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+