-
Rute 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Patapita nthawi, ana awiriwo, Maloni ndi Kiliyoni, nawonso anamwalira, moti Naomi anatsala yekha wopanda ana ake awiri aja, komanso wopanda mwamuna.
-