Deuteronomo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira. Deuteronomo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova adzachulukitsa chuma chako pa zipatso za mimba yako,+ zipatso za ziweto zako ndi zipatso za m’munda mwako,+ m’dziko limene Yehova analumbirira makolo ako kuti adzakupatsa.+
31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira.
11 “Yehova adzachulukitsa chuma chako pa zipatso za mimba yako,+ zipatso za ziweto zako ndi zipatso za m’munda mwako,+ m’dziko limene Yehova analumbirira makolo ako kuti adzakupatsa.+