Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo pa nthawi ya chakudya Boazi anaitana Rute kuti: “Tabwera kuno udzadye mkate+ ndiponso uziusunsa mu vinyo wowawasayu.” Choncho Rute anadzakhala pansi limodzi ndi okololawo, ndipo Boazi anali kum’patsira mbewu zokazinga,+ iye n’kumadya moti anakhuta mpaka zina kutsala.

  • Yohane 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu onsewo atakhuta,+ iye anauza ophunzira ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke chilichonse.”

  • 1 Timoteyo 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma ngati mkazi wamasiye aliyense ali ndi ana kapena adzukulu, amenewo aphunzire kukhala odzipereka kwa Mulungu m’banja mwawo choyamba,+ mwa kubwezera kwa makolo+ ndi agogo awo zowayenerera, pakuti zimenezi zimakondweretsa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena