Yoswa 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+ Yoswa 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ana a Yosefe anati: “Dera lamapiri silitikwanira, ndiponso Akanani a kuchigwa, a ku Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira, ndiponso a kuchigwa cha Yezereeli,+ ali ndi magaleta ankhondo+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.”
5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+
16 Kenako ana a Yosefe anati: “Dera lamapiri silitikwanira, ndiponso Akanani a kuchigwa, a ku Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira, ndiponso a kuchigwa cha Yezereeli,+ ali ndi magaleta ankhondo+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.”