Genesis 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele, ndipo anam’konda kwambiri Rakele kuposa Leya.+ Motero anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+ Deuteronomo 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mwamuna akakhala ndi akazi awiri, wina wokondedwa ndi wina wosakondedwa, ndipo onse awiri, wokondedwa ndi wosakondedwayo, abereka ana aamuna ndi mwamunayo, koma mwana wa mkazi wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa,+
30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele, ndipo anam’konda kwambiri Rakele kuposa Leya.+ Motero anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+
15 “Mwamuna akakhala ndi akazi awiri, wina wokondedwa ndi wina wosakondedwa, ndipo onse awiri, wokondedwa ndi wosakondedwayo, abereka ana aamuna ndi mwamunayo, koma mwana wa mkazi wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa,+