Yoswa 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo amunawo atuluka usiku uno nthawi yotseka chipata+ itayandikira. Koma ine sindikudziwa kumene alowera. Fulumirani! Athamangireni! Muwapeza amenewo.” Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
5 Ndipo amunawo atuluka usiku uno nthawi yotseka chipata+ itayandikira. Koma ine sindikudziwa kumene alowera. Fulumirani! Athamangireni! Muwapeza amenewo.”
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+