Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo wansembe azitentha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi. Mafuta onse ndi a Yehova.+

  • Levitiko 7:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pakuti aliyense wodya mafuta a nyama imene waipereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto, munthu ameneyo aziphedwa+ kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.

  • Levitiko 7:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno wansembe azitentha mafutawo+ paguwa lansembe, koma ngangayo izikhala ya Aroni ndi ana ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena