1 Samueli 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Yonatani, mwana wa Sauli, anali kukonda kwambiri Davide.+ Choncho Yonatani anauza Davide kuti: “Sauli, bambo anga, akufuna kukupha. Chonde, mawa m’mawa ukhale wosamala. Ukakhale pamalo obisika ndipo ukabisalebe choncho.+ Miyambo 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala,+ koma anthu osadziwa zinthu amangopitabe ndipo amalangidwa.+
2 Koma Yonatani, mwana wa Sauli, anali kukonda kwambiri Davide.+ Choncho Yonatani anauza Davide kuti: “Sauli, bambo anga, akufuna kukupha. Chonde, mawa m’mawa ukhale wosamala. Ukakhale pamalo obisika ndipo ukabisalebe choncho.+
3 Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala,+ koma anthu osadziwa zinthu amangopitabe ndipo amalangidwa.+