1 Samueli 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Samueli anachita zimene Yehova anamuuza. Atafika ku Betelehemu,+ akulu a mzindawo anayamba kunjenjemera+ atakumana naye. Ndiyeno iwo anati: “Kodi n’kwabwino?”+ 1 Samueli 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mmodzi mwa atumikiwo anayankha, kuti: “Inetu ndinaona luso loimba+ la mwana wa Jese wa ku Betelehemu. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso wamphamvu,+ mwamuna wankhondo,+ wolankhula mwanzeru+ ndi wooneka bwino,+ komanso Yehova ali naye.”+ Yohane 7:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+
4 Samueli anachita zimene Yehova anamuuza. Atafika ku Betelehemu,+ akulu a mzindawo anayamba kunjenjemera+ atakumana naye. Ndiyeno iwo anati: “Kodi n’kwabwino?”+
18 Mmodzi mwa atumikiwo anayankha, kuti: “Inetu ndinaona luso loimba+ la mwana wa Jese wa ku Betelehemu. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso wamphamvu,+ mwamuna wankhondo,+ wolankhula mwanzeru+ ndi wooneka bwino,+ komanso Yehova ali naye.”+
42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+