Ekisodo 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Katatu pa chaka, mwamuna aliyense pakati panu azionekera+ kwa Ambuye woona, Yehova, Mulungu wa Isiraeli. Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+ Yoswa 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsopano chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu,+ ndipo tembenuzirani mitima yanu kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.”
23 “Katatu pa chaka, mwamuna aliyense pakati panu azionekera+ kwa Ambuye woona, Yehova, Mulungu wa Isiraeli.
23 “Tsopano chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu,+ ndipo tembenuzirani mitima yanu kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.”