Yobu 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi iye saona njira zanga,+Ndi kuwerenga masitepe anga onse? Salimo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+ Salimo 139:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 139 Inu Yehova, mwandifufuza ndipo mukundidziwa.+
3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+