1 Samueli 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 N’chifukwa chiyani anthu inu mukunyozabe nsembe zanga+ zimene ndinalamula m’nyumba yanga,+ n’kumalemekezabe ana anu koposa ine mwa kudzinenepetsa+ ndi mbali yabwino kwambiri ya nsembe iliyonse ya anthu anga Aisiraeli?+ Yesaya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene akutsogolera anthuwa ndiwo amene akuwasocheretsa,+ ndipo amene akutsogoleredwawo ndiwo amene akusokonezedwa.+
29 N’chifukwa chiyani anthu inu mukunyozabe nsembe zanga+ zimene ndinalamula m’nyumba yanga,+ n’kumalemekezabe ana anu koposa ine mwa kudzinenepetsa+ ndi mbali yabwino kwambiri ya nsembe iliyonse ya anthu anga Aisiraeli?+
16 Amene akutsogolera anthuwa ndiwo amene akuwasocheretsa,+ ndipo amene akutsogoleredwawo ndiwo amene akusokonezedwa.+