Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tizilombo timeneti n’timene mungadzidetse nato. Aliyense wokhudza zolengedwa zimenezi zitafa azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+

  • Levitiko 15:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komanso munthu wokhudza bedi lakelo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+

  • Levitiko 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Mwamuna akatulutsa umuna,+ azisamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.

  • Levitiko 15:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “‘Mkazi akagonana ndi mwamuna, onse awiri azisamba thupi lonse, ndipo azikhala odetsedwa+ kufikira madzulo.

  • Numeri 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aliyense amene wakhudza mtembo wa munthu amene waphedwa ndi lupanga,+ kapena mtembo uliwonse, kapenanso fupa la munthu,+ ngakhalenso manda a munthu, akhale wodetsedwa masiku 7.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena