Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Miyambo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usamagwirizane ndi munthu aliyense wokonda kukwiya,+ ndipo usamayende ndi munthu waukali,
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+