1 Samueli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anakhala mtumiki+ wa Yehova pamaso pa wansembe Eli. 1 Samueli 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Samueli anagonabe mpaka m’mawa. Atadzuka anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova,+ koma anaopa kuuza Eli za masomphenya amene anaona.+ Miyambo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhale mnyamata amadziwika ndi ntchito zake, ngati zochita zake zili zoyera ndiponso zowongoka.+
11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anakhala mtumiki+ wa Yehova pamaso pa wansembe Eli.
15 Ndiyeno Samueli anagonabe mpaka m’mawa. Atadzuka anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova,+ koma anaopa kuuza Eli za masomphenya amene anaona.+
11 Ngakhale mnyamata amadziwika ndi ntchito zake, ngati zochita zake zili zoyera ndiponso zowongoka.+