-
Maliko 2:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 M’nkhani yonena za Abiyatara+ wansembe wamkulu, Davide analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa+ kwa Mulungu. Anatenga mitanda ina ya mkatewo n’kupatsanso amuna amene anali naye limodzi.+ Oyenera kudya mkate umenewu ndi ansembe okha basi ndipo anthu ena onse saloledwa kudya.+ Kodi inu simunawerenge nkhani imeneyi?”
-