Genesis 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Zitatero, Abulahamu anabzala mtengo wa bwemba pa Beere-seba, n’kuitanirapo dzina la Yehova,+ Mulungu wanthawi zonse.+ 1 Samueli 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atatero, anatenga mafupa awo+ ndi kuwaika m’manda+ pansi pa mtengo wa bwemba+ ku Yabesi. Pambuyo pake, anasala kudya masiku 7.+ 1 Mbiri 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero amuna onse olimba mtima ananyamuka n’kukanyamula mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake n’kupita nayo ku Yabesi. Atatero anakafotsera mafupa awo pansi pa mtengo waukulu+ ku Yabesiko.+ Kenako anasala kudya+ masiku 7.
33 Zitatero, Abulahamu anabzala mtengo wa bwemba pa Beere-seba, n’kuitanirapo dzina la Yehova,+ Mulungu wanthawi zonse.+
13 Atatero, anatenga mafupa awo+ ndi kuwaika m’manda+ pansi pa mtengo wa bwemba+ ku Yabesi. Pambuyo pake, anasala kudya masiku 7.+
12 Chotero amuna onse olimba mtima ananyamuka n’kukanyamula mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake n’kupita nayo ku Yabesi. Atatero anakafotsera mafupa awo pansi pa mtengo waukulu+ ku Yabesiko.+ Kenako anasala kudya+ masiku 7.