1 Samueli 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+ 1 Samueli 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Davide anauza Ahimeleki wansembe kuti: “Mfumu yandituma nkhani inayake,+ ndipo yandiuza kuti, ‘Usauze munthu aliyense nkhani imene ndikukutuma ndi zimene ndakulamula.’ Choncho ndapangana ndi anyamata kuti ndikumane nawo pamalo enaake.
21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+
2 Pamenepo Davide anauza Ahimeleki wansembe kuti: “Mfumu yandituma nkhani inayake,+ ndipo yandiuza kuti, ‘Usauze munthu aliyense nkhani imene ndikukutuma ndi zimene ndakulamula.’ Choncho ndapangana ndi anyamata kuti ndikumane nawo pamalo enaake.