1 Samueli 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano tsiku limenelo, mmodzi wa atumiki a Sauli, dzina lake Doegi,+ Mwedomu,+ anali kumeneko chifukwa anali atamusunga+ pamaso pa Yehova. Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.+
7 Tsopano tsiku limenelo, mmodzi wa atumiki a Sauli, dzina lake Doegi,+ Mwedomu,+ anali kumeneko chifukwa anali atamusunga+ pamaso pa Yehova. Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.+