-
Oweruza 6:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Komabe, Gidiyoni anauza Mulungu woona kuti: “Mkwiyo wanu usandiyakire chonde, ndiloleni ndilankhulenso kamodzi kokhaka. Ndiloleni chonde, ndikuyeseninso kamodzi kokha ndi ubweyawu, kuti nditsimikizire za nkhaniyi. Nthaka yonse ikhathamire ndi mame, koma ubweya wokhawu ukhale wouma.”
-