Salimo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Yeremiya 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Mundiitane ndipo ndidzakuyankhani.+ Nthawi yomweyo ndidzakuuzani zinthu zazikulu ndi zovuta kuzimvetsa zimene simukuzidziwa.’”+
6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+
3 ‘Mundiitane ndipo ndidzakuyankhani.+ Nthawi yomweyo ndidzakuuzani zinthu zazikulu ndi zovuta kuzimvetsa zimene simukuzidziwa.’”+