1 Samueli 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anakanthanso ndi lupanga Nobu,+ mzinda wa ansembe. Anapha amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa, komanso ng’ombe zamphongo, abulu ndi nkhosa. Miyambo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtsogoleri woipa wolamulira anthu onyozeka ali ngati mkango wobangula ndiponso chimbalangondo chimene chikubwera kudzakuluma.+
19 Iye anakanthanso ndi lupanga Nobu,+ mzinda wa ansembe. Anapha amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa, komanso ng’ombe zamphongo, abulu ndi nkhosa.
15 Mtsogoleri woipa wolamulira anthu onyozeka ali ngati mkango wobangula ndiponso chimbalangondo chimene chikubwera kudzakuluma.+