Salimo 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.] Salimo 70:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+ Miyambo 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu ambiri amafuna kuonana ndi mtsogoleri,+ koma chiweruzo cha munthu chimachokera kwa Yehova.+
3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]
2 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+