Genesis 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero Abulamu anagona ndi Hagara ndipo Hagara anatenga pakati. Hagara atazindikira kuti ali ndi pakati, anayamba kuchitira chipongwe mbuye wake Sarai.+
4 Chotero Abulamu anagona ndi Hagara ndipo Hagara anatenga pakati. Hagara atazindikira kuti ali ndi pakati, anayamba kuchitira chipongwe mbuye wake Sarai.+