1 Samueli 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova adzabwezera aliyense malinga ndi chilungamo+ ndi kukhulupirika kwake, pakuti lero Yehova anakuperekani m’manja mwanga, koma sindinafune kutambasula dzanja langa ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Salimo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+
23 Yehova adzabwezera aliyense malinga ndi chilungamo+ ndi kukhulupirika kwake, pakuti lero Yehova anakuperekani m’manja mwanga, koma sindinafune kutambasula dzanja langa ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+
8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+