Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Yonatani anati: “N’zosatheka kuti iwe ukhale wolakwa! Koma ngati ndingadziwe zoipa zimene bambo anga akufuna kukuchitira, ukuganiza kuti sindingakuuze?”+

  • 1 Samueli 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nthawi yomweyo, Davide anauza amuna amene anali kuyenda naye kuti: “Aliyense amange lupanga lake m’chiuno!”+ Pamenepo aliyense anamangadi lupanga lake m’chiuno, ndipo Davide nayenso anamanga lupanga lake m’chiuno. Zitatero, amuna pafupifupi 400 anapitira limodzi ndi Davide, koma amuna 200 anatsala kuti ayang’anire katundu.+

  • Esitere 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno mfumu inanyamuka mokwiya+ kuchoka paphwando la vinyo ndi kupita kumunda wamaluwa wa panyumba ya mfumu. Pamenepo Hamani ananyamuka kuti apemphe Mfumukazi Esitere kuti ipulumutse moyo wake,+ chifukwa anaona kuti mfumu yatsimikiza zomupatsa chilango.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena