Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 11:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yehova analola mitunduyo kuumitsa mitima+ yawo kuti ichite nkhondo ndi Aisiraeli. Anatero kuti iye awawononge ndi kuti Aisiraeliwo asawamvere chisoni,+ koma kuti awatheretu monga mmene Yehova analamulira Mose.+

  • Yobu 34:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+

      Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake.

  • Miyambo 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munthu wosiya njira yabwino amadana ndi malangizo.+ Aliyense wodana ndi chidzudzulo adzafa.+

  • Aroma 9:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+

  • Aheberi 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 M’malomwake, pitirizani kudandaulirana+ tsiku ndi tsiku, nthawi iliyonse imene mukuti “Lero,”+ kuopera kuti chinyengo+ champhamvu cha uchimo chingaumitse mtima wa wina wa inu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena