Oweruza 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova anatumiza munthu wina, mneneri,+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anawauza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndine amene ndinakutulutsani mu Iguputo,+ m’nyumba yaukapolo.+ Aheberi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+
8 Yehova anatumiza munthu wina, mneneri,+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anawauza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndine amene ndinakutulutsani mu Iguputo,+ m’nyumba yaukapolo.+
1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+