1 Mbiri 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anati: ‘Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.’+ Salimo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,+Amamupulumutsa ndi dzanja lake lamanja lamphamvu zopulumutsa.+ Salimo 105:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+
22 Iye anati: ‘Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.’+
6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,+Amamupulumutsa ndi dzanja lake lamanja lamphamvu zopulumutsa.+
15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+