Ekisodo 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mkazi wamatsenga musam’lole kukhala ndi moyo.+ Levitiko 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+
27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+