2 Atesalonika 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndi kusalungama ndi chinyengo chilichonse.+ Zonsezi adzazichita kwa amene akupita kukawonongedwa.+ Izi zidzakhala chilango kwa iwo chifukwa sanasonyeze kuti akulakalaka+ choonadi, kuti apulumuke.+ 2 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+
10 ndi kusalungama ndi chinyengo chilichonse.+ Zonsezi adzazichita kwa amene akupita kukawonongedwa.+ Izi zidzakhala chilango kwa iwo chifukwa sanasonyeze kuti akulakalaka+ choonadi, kuti apulumuke.+