Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Samueli anati: “N’chiyani chimene wachita?”+ Poyankha Sauli anati: “Nditaona kuti anthu akubalalika kundisiya ndekha,+ ndipo inu simunabwere m’masiku amene munanena aja,+ komanso kuti Afilisiti anali kusonkhana pamodzi ku Mikimasi,+

  • 1 Mbiri 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena