Genesis 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Abulahamu anathamangira kumene kunali ziweto, n’kutengako ng’ombe yaing’ono yamphongo yonona. Atatero, anaipereka kwa wantchito wake, ndipo iye anaikonza mwamsanga.+ Luka 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mubweretse mwana wa ng’ombe wamphongo wonenepa,+ mumuphe ndipo tidye tisangalale.
7 Kenako, Abulahamu anathamangira kumene kunali ziweto, n’kutengako ng’ombe yaing’ono yamphongo yonona. Atatero, anaipereka kwa wantchito wake, ndipo iye anaikonza mwamsanga.+