1 Samueli 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Davide ananyamuka tsiku limenelo, ndipo anapitiriza kuthawa+ chifukwa choopa Sauli. Patapita nthawi anafika kwa Akisi mfumu ya Gati.+ 1 Samueli 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Davide pamodzi ndi amuna 600+ amene anali kuyenda naye ananyamuka ndi kupita kwa Akisi+ mfumu ya Gati, mwana wa Maoki.
10 Pamenepo Davide ananyamuka tsiku limenelo, ndipo anapitiriza kuthawa+ chifukwa choopa Sauli. Patapita nthawi anafika kwa Akisi mfumu ya Gati.+
2 Choncho Davide pamodzi ndi amuna 600+ amene anali kuyenda naye ananyamuka ndi kupita kwa Akisi+ mfumu ya Gati, mwana wa Maoki.