Numeri 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+ Salimo 121:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzakuteteza pa zochita zako zonse,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+
17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+