Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 5:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 ‘Kodi sanapeze zofunkha ndipo ayenera kuzigawa?+

      Kodi sayenera kugawa mkazi mmodzi, kapenanso akazi awiri kwa mwamuna aliyense wamphamvu,+

      Ndi nsalu za Sisera zofunkhidwa zonyika mu utoto, ndithu nsalu zofunkhidwa zonyika mu utoto?

      Kodi sayenera kugawa chovala chopeta chonyika mu utoto, inde, zovala ziwiri zopeta,

      Kuti amuna ofunkha avale m’makosi awo?’

  • 1 Samueli 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Davide anapitiriza kukhala ndi Akisi ku Gati. Iye anakhala kumeneko pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye, ndipo aliyense mwa amunawo anali ndi banja lake.+ Davide anali ndi akazi ake awiri aja, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena