1 Mafumu 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Solomo anathamangitsa Abiyatara n’kumusiyitsa kutumikira monga wansembe wa Yehova, pokwaniritsa mawu amene Yehova analankhula ku Silo,+ otsutsana ndi nyumba ya Eli.+
27 Choncho Solomo anathamangitsa Abiyatara n’kumusiyitsa kutumikira monga wansembe wa Yehova, pokwaniritsa mawu amene Yehova analankhula ku Silo,+ otsutsana ndi nyumba ya Eli.+