1 Mbiri 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chuma+ ndi ulemerero+ zimachokera kwa inu. Inu mumalamulira+ chilichonse. M’dzanja lanu muli mphamvu+ ndi nyonga,+ ndipo dzanja lanu limatha kukweza+ ndiponso kupereka mphamvu kwa onse.+ Salimo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
12 Chuma+ ndi ulemerero+ zimachokera kwa inu. Inu mumalamulira+ chilichonse. M’dzanja lanu muli mphamvu+ ndi nyonga,+ ndipo dzanja lanu limatha kukweza+ ndiponso kupereka mphamvu kwa onse.+
16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+