1 Samueli 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Pamenepo anamuyankha+ kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapezadi ndi kulanditsa zinthu zimene afunkha.”+ Salimo 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+
8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Pamenepo anamuyankha+ kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapezadi ndi kulanditsa zinthu zimene afunkha.”+
3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+