Oweruza 9:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Msangamsanga Abimeleki anaitana mtumiki wake womunyamulira zida ndi kumuuza kuti: “Tenga lupanga lako undiphe,+ kuopera kuti anthu anganene za ine kuti, ‘Anaphedwa ndi mkazi.’” Nthawi yomweyo, mtumiki wakeyo anamubaya* ndi lupanga, ndipo anafa.+ 1 Mbiri 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Sauli anauza womunyamulira zida+ kuti: “Solola lupanga lako+ undibaye* nalo, kuti amuna osadulidwawa+ asandipeze ndi kundizunza.”+ Koma womunyamulira zida uja sanafune+ kuchita zimenezo, chifukwa anali kuchita mantha kwambiri. Chotero Sauli anatenga lupanga lake n’kuligwera.+
54 Msangamsanga Abimeleki anaitana mtumiki wake womunyamulira zida ndi kumuuza kuti: “Tenga lupanga lako undiphe,+ kuopera kuti anthu anganene za ine kuti, ‘Anaphedwa ndi mkazi.’” Nthawi yomweyo, mtumiki wakeyo anamubaya* ndi lupanga, ndipo anafa.+
4 Kenako Sauli anauza womunyamulira zida+ kuti: “Solola lupanga lako+ undibaye* nalo, kuti amuna osadulidwawa+ asandipeze ndi kundizunza.”+ Koma womunyamulira zida uja sanafune+ kuchita zimenezo, chifukwa anali kuchita mantha kwambiri. Chotero Sauli anatenga lupanga lake n’kuligwera.+